Yesaya 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yehova wanena kuti: “Kodi nsembe zanu zambirimbirizo zili ndi phindu lanji kwa ine?+ Nsembe zanu zopsereza za nkhosa zamphongo+ ndiponso mafuta a nyama zodyetsedwa bwino+ zandikwana.Sindikusangalala ndi magazi+ a ngʼombe zazingʼono zamphongo,+ a ana a nkhosa ndiponso magazi a mbuzi.+
11 Yehova wanena kuti: “Kodi nsembe zanu zambirimbirizo zili ndi phindu lanji kwa ine?+ Nsembe zanu zopsereza za nkhosa zamphongo+ ndiponso mafuta a nyama zodyetsedwa bwino+ zandikwana.Sindikusangalala ndi magazi+ a ngʼombe zazingʼono zamphongo,+ a ana a nkhosa ndiponso magazi a mbuzi.+