Hoseya 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ngakhale kuti inu Aisiraeli mukuchita chiwerewere,+Yuda asakhale ndi mlandu.+ Musabwere ku Giligala+ kapena ku Beti-aveni,+Ndipo musalumbire kuti, ‘Mʼdzina la Yehova Mulungu wamoyo!’+ Hoseya 12:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ku Giliyadi anthu akuchita zachinyengo*+ ndiponso akulankhula mabodza. Ku Giligala, akupereka nsembe ngʼombe zamphongo.+Ndipo maguwa awo ansembe ali ngati milu yamiyala mʼmunda.+ Amosi 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Musakhale ndi mtima wofuna kupita ku Beteli.+Ndipo musapite ku Giligala+ kapena ku Beere-seba.+Chifukwa ndithu Giligala adzapita ku ukapolo.+Ndipo Beteli adzawonongedwa.*
15 Ngakhale kuti inu Aisiraeli mukuchita chiwerewere,+Yuda asakhale ndi mlandu.+ Musabwere ku Giligala+ kapena ku Beti-aveni,+Ndipo musalumbire kuti, ‘Mʼdzina la Yehova Mulungu wamoyo!’+
11 Ku Giliyadi anthu akuchita zachinyengo*+ ndiponso akulankhula mabodza. Ku Giligala, akupereka nsembe ngʼombe zamphongo.+Ndipo maguwa awo ansembe ali ngati milu yamiyala mʼmunda.+
5 Musakhale ndi mtima wofuna kupita ku Beteli.+Ndipo musapite ku Giligala+ kapena ku Beere-seba.+Chifukwa ndithu Giligala adzapita ku ukapolo.+Ndipo Beteli adzawonongedwa.*