Hoseya 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mayiyu ndidzamudzala ngati mbewu zanga padziko lapansi.+Ndidzachitira chifundo amene sanasonyezedwe chifundo.*Ndipo ndidzauza anthu amene si anthu anga kuti: “Ndinu anthu anga,”*+ Iwo adzayankha kuti: “Inu ndinu Mulungu wathu.”’”+
23 Mayiyu ndidzamudzala ngati mbewu zanga padziko lapansi.+Ndidzachitira chifundo amene sanasonyezedwe chifundo.*Ndipo ndidzauza anthu amene si anthu anga kuti: “Ndinu anthu anga,”*+ Iwo adzayankha kuti: “Inu ndinu Mulungu wathu.”’”+