Deuteronomo 16:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Muzichita zinthu mwachilungamo+ kuti mukhale ndi moyo nʼkukatenga dziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani. Mika 6:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iye anakuuza munthu iwe zimene zili zabwino. Kodi Yehova akufuna kuti uzichita* chiyani? Iye akungofuna kuti uzichita chilungamo,*+ uziona kuti kukhulupirika nʼkofunika,*+Ndiponso uziyenda modzichepetsa+ ndi Mulungu wako.+
20 Muzichita zinthu mwachilungamo+ kuti mukhale ndi moyo nʼkukatenga dziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani.
8 Iye anakuuza munthu iwe zimene zili zabwino. Kodi Yehova akufuna kuti uzichita* chiyani? Iye akungofuna kuti uzichita chilungamo,*+ uziona kuti kukhulupirika nʼkofunika,*+Ndiponso uziyenda modzichepetsa+ ndi Mulungu wako.+