Genesis 29:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma Yakobo anakonda Rakele, ndiye anati: “Ndine wokonzeka kukugwirirani ntchito zaka 7, kuti mudzandipatse Rakele mwana wanu wamngʼonoyu.”+
18 Koma Yakobo anakonda Rakele, ndiye anati: “Ndine wokonzeka kukugwirirani ntchito zaka 7, kuti mudzandipatse Rakele mwana wanu wamngʼonoyu.”+