Oweruza 8:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Gidiyoni anatenga golideyo nʼkupanga chovala cha efodi,+ ndipo anachiika pamalo oonekera mumzinda wakwawo wa Ofira.+ Aisiraeli onse anayamba kuchilambira,*+ moti chinakhala msampha kwa Gidiyoni ndi anthu a mʼbanja lake.+
27 Gidiyoni anatenga golideyo nʼkupanga chovala cha efodi,+ ndipo anachiika pamalo oonekera mumzinda wakwawo wa Ofira.+ Aisiraeli onse anayamba kuchilambira,*+ moti chinakhala msampha kwa Gidiyoni ndi anthu a mʼbanja lake.+