Ezekieli 23:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Iwo achita chigololo*+ ndipo mʼmanja mwawo muli magazi. Kuwonjezera pa kuchita chigololo ndi mafano awo onyansa, iwo awotcha pamoto ana awo aamuna amene anandiberekera kuti akhale chakudya cha mafano awowo.+
37 Iwo achita chigololo*+ ndipo mʼmanja mwawo muli magazi. Kuwonjezera pa kuchita chigololo ndi mafano awo onyansa, iwo awotcha pamoto ana awo aamuna amene anandiberekera kuti akhale chakudya cha mafano awowo.+