Ezekieli 34:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ndidzawapatsa munda umene udzakhale wotchuka* chifukwa cha mbewu zake ndipo anthu sadzafanso ndi njala mʼdzikomo+ komanso anthu a mitundu ina sadzawanyozanso.+ Ezekieli 36:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 ‘Sindidzachititsanso kuti anthu a mitundu ina azikunyozani kapena kuti anthu azikunenerani mawu achipongwe+ ndipo simudzakhumudwitsanso mitundu ya anthu amene akukhala mwa inu,’ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”
29 Ndidzawapatsa munda umene udzakhale wotchuka* chifukwa cha mbewu zake ndipo anthu sadzafanso ndi njala mʼdzikomo+ komanso anthu a mitundu ina sadzawanyozanso.+
15 ‘Sindidzachititsanso kuti anthu a mitundu ina azikunyozani kapena kuti anthu azikunenerani mawu achipongwe+ ndipo simudzakhumudwitsanso mitundu ya anthu amene akukhala mwa inu,’ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”