-
Ezekieli 37:26, 27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 Ndidzachita nawo pangano lamtendere+ ndipo pangano limeneli lidzakhalapo mpaka kalekale. Ine ndidzachititsa kuti akhazikike mʼdzikolo ndipo ndidzawachulukitsa+ komanso ndidzaika malo anga opatulika pakati pawo mpaka kalekale. 27 Tenti yanga idzakhala* pakati pawo.* Ine ndidzakhala Mulungu wawo ndipo iwo adzakhala anthu anga.+
-