-
Yesaya 60:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
Mipanda yako udzaitcha Chipulumutso+ ndipo mageti ako udzawatcha Tamanda.
-
-
Zekariya 14:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Mphika uliwonse wakukamwa kwakukulu mu Yerusalemu ndi mu Yuda udzakhala woyera ndipo udzakhala wa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba. Anthu onse amene azidzapereka nsembe azidzatenga ina mwa miphikayo nʼkuphikiramo. Pa tsiku limenelo, mʼnyumba ya Yehova wa magulu ankhondo akumwamba simudzapezeka munthu wa ku Kanani.”*+
-