18 Iwo ananena kuti: “Tabwerani, tiyeni timukonzere chiwembu Yeremiya,+ chifukwa ansembe adzapitiriza kutiphunzitsa chilamulo. Anthu athu anzeru sadzasiya kutipatsa malangizo ndipo aneneri adzapitiriza kutiuza mawu a Mulungu. Bwerani, tiyeni titsutsane naye ndipo tisamvere zimene akunena.”