Amosi 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Musakhale ndi mtima wofuna kupita ku Beteli.+Ndipo musapite ku Giligala+ kapena ku Beere-seba.+Chifukwa ndithu Giligala adzapita ku ukapolo.+Ndipo Beteli adzawonongedwa.* Amosi 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anthu amenewa adzakhala oyambirira kupita ku ukapolo,+Ndipo phwando laphokoso la anthu ogona modziwongola pamipando yokhala ngati bedi lidzatha.
5 Musakhale ndi mtima wofuna kupita ku Beteli.+Ndipo musapite ku Giligala+ kapena ku Beere-seba.+Chifukwa ndithu Giligala adzapita ku ukapolo.+Ndipo Beteli adzawonongedwa.*
7 Anthu amenewa adzakhala oyambirira kupita ku ukapolo,+Ndipo phwando laphokoso la anthu ogona modziwongola pamipando yokhala ngati bedi lidzatha.