Yeremiya 11:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Choncho izi ndi zimene Yehova wanena zokhudza anthu a ku Anatoti+ amene akufuna kuchotsa moyo wako, ndipo akunena kuti: “Usanenere mʼdzina la Yehova+ ngati ukufuna kuti tisakuphe.” Amosi 7:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma usapitirize kunenera ku Beteli kuno,+ chifukwa ndi malo opatulika a mfumu+ ndiponso nyumba ya ufumuwu.”
21 Choncho izi ndi zimene Yehova wanena zokhudza anthu a ku Anatoti+ amene akufuna kuchotsa moyo wako, ndipo akunena kuti: “Usanenere mʼdzina la Yehova+ ngati ukufuna kuti tisakuphe.”
13 Koma usapitirize kunenera ku Beteli kuno,+ chifukwa ndi malo opatulika a mfumu+ ndiponso nyumba ya ufumuwu.”