Yoweli 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Komanso kodi ndakulakwira chiyaniIwe Turo ndi Sidoni ndiponso nonse amʼchigawo cha Filisitiya? Kodi mukundichitira zimenezi pondibwezera zimene ndinachita? Ngati mukundibwezera,Ine ndidzakubwezerani mwamsanga ndiponso mofulumira zimene mwandichitirazo.+ Yoweli 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Komanso mwagulitsa anthu a ku Yuda ndi a ku Yerusalemu kwa Agiriki,+Kuti muwapititse kutali ndi dziko lawo,
4 Komanso kodi ndakulakwira chiyaniIwe Turo ndi Sidoni ndiponso nonse amʼchigawo cha Filisitiya? Kodi mukundichitira zimenezi pondibwezera zimene ndinachita? Ngati mukundibwezera,Ine ndidzakubwezerani mwamsanga ndiponso mofulumira zimene mwandichitirazo.+
6 Komanso mwagulitsa anthu a ku Yuda ndi a ku Yerusalemu kwa Agiriki,+Kuti muwapititse kutali ndi dziko lawo,