Yobu 36:27, 28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Iye amakoka madontho a madzi.+Madonthowo amasintha nʼkukhala nkhungu imene imapanga mvula,28 Kenako mitambo imagwetsa mvula,+Imagwetsera aliyense madzi. Salimo 135:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Amachititsa kuti mitambo* ikwere kuchokera kumalekezero a dziko lapansi.Iye amachititsa kuti kukamagwa mvula mphezi zizingʼanima.Amatulutsa mphepo kuchokera mʼnyumba zake zosungira zinthu.+
27 Iye amakoka madontho a madzi.+Madonthowo amasintha nʼkukhala nkhungu imene imapanga mvula,28 Kenako mitambo imagwetsa mvula,+Imagwetsera aliyense madzi.
7 Amachititsa kuti mitambo* ikwere kuchokera kumalekezero a dziko lapansi.Iye amachititsa kuti kukamagwa mvula mphezi zizingʼanima.Amatulutsa mphepo kuchokera mʼnyumba zake zosungira zinthu.+