-
Ezekieli 25:8, 9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Chifukwa chakuti Mowabu+ ndi Seiri+ anena kuti, “Taonani! Nyumba ya Yuda ili ngati mitundu ina yonse ya anthu,” 9 ine ndidzachititsa kuti adani aukire mizinda imene ili mʼmalire mwa Mowabu,* kuphatikizapo mizinda yake yabwino kwambiri.* Mizindayo ndi Beti-yesimoti, Baala-meoni mpaka kukafika ku Kiriyataimu.+
-