8 Yehova, Mulungu wa magulu ankhondo akumwamba, wanena kuti: ‘Ine Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, ndalumbira pa dzina langaʼ+ kuti,
‘Ndimanyasidwa ndi kunyada kwa Yakobo,+
Ndimadana ndi nsanja zake zolimba,+
Ndipo ndidzapereka mzindawu ndi zinthu zake zonse kwa adani ake.+