Yeremiya 49:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Chifukwa ine ndalumbira pa dzina langa kuti Bozira adzakhala chinthu chochititsa mantha,+ adzanyozedwa, adzawonongedwa ndi kutembereredwa ndipo mizinda yake yonse idzakhala mabwinja mpaka kalekale,” akutero Yehova.+
13 “Chifukwa ine ndalumbira pa dzina langa kuti Bozira adzakhala chinthu chochititsa mantha,+ adzanyozedwa, adzawonongedwa ndi kutembereredwa ndipo mizinda yake yonse idzakhala mabwinja mpaka kalekale,” akutero Yehova.+