Salimo 137:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Inu Yehova, kumbukiraniZimene Aedomu ananena pa tsiku limene Yerusalemu anawonongedwa. Iwo anati: “Gwetsani mzindawo! Ugwetseni mpaka pamaziko ake!”+ Ezekieli 25:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Edomu wabwezera zoipa kwa nyumba ya Yuda ndipo wapalamula mlandu waukulu chifukwa chowabwezera.+
7 Inu Yehova, kumbukiraniZimene Aedomu ananena pa tsiku limene Yerusalemu anawonongedwa. Iwo anati: “Gwetsani mzindawo! Ugwetseni mpaka pamaziko ake!”+
12 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Edomu wabwezera zoipa kwa nyumba ya Yuda ndipo wapalamula mlandu waukulu chifukwa chowabwezera.+