Yesaya 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Aliyense amene adzatsale mu Ziyoni ndiponso amene adzasiyidwe mu Yerusalemu adzatchedwa woyera, anthu onse a mu Yerusalemu amene analembedwa mayina kuti akhale ndi moyo.+ Zekariya 8:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Yehova wanena kuti, ‘Ndidzabwerera ku Ziyoni+ ndipo ndizidzakhala ku Yerusalemu.+ Yerusalemu adzatchedwa mzinda wa choonadi*+ ndipo phiri la Yehova wa magulu ankhondo akumwamba lidzatchedwa phiri loyera.’”+
3 Aliyense amene adzatsale mu Ziyoni ndiponso amene adzasiyidwe mu Yerusalemu adzatchedwa woyera, anthu onse a mu Yerusalemu amene analembedwa mayina kuti akhale ndi moyo.+
3 “Yehova wanena kuti, ‘Ndidzabwerera ku Ziyoni+ ndipo ndizidzakhala ku Yerusalemu.+ Yerusalemu adzatchedwa mzinda wa choonadi*+ ndipo phiri la Yehova wa magulu ankhondo akumwamba lidzatchedwa phiri loyera.’”+