-
1 Mafumu 19:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Yezebeli atamva zimenezo, anatuma munthu kwa Eliya kukamuuza kuti: “Milungu yanga indilange mowirikiza, ngati pofika nthawi ino mawa sindidzakhala nditakupha ngati mmene waphera aneneriwo.”
-
-
Yobu 6:8, 9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Zikanakhala bwino zimene ndapempha zikanachitika,
Ndiponso Mulungu akanandipatsa zimene ndikufuna.
-