Levitiko 26:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndikadzawononga njira* zanu zopezera chakudya,+ akazi 10 adzaphika mkate mu uvuni umodzi wokha, ndipo pokugawirani mkatewo, adzachita kukuyezerani+ nʼkukupatsani wochepa. Choncho mudzadya koma simudzakhuta.+ Ezekieli 4:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kenako anandiuza kuti: “Iwe mwana wa munthu, ine ndidzachititsa kuti chakudya chisowe* mu Yerusalemu.+ Anthu azidzadya chakudya chochita kuyeza ndipo adzachidya ali ndi nkhawa yaikulu.+ Azidzamwa madzi ochita kuyeza ali ndi mantha aakulu.+ Hoseya 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iwo adzadya, koma sadzakhuta.+ Adzachita zachiwerewere, koma sadzachulukana,+Chifukwa chakuti sakumvera Yehova.
26 Ndikadzawononga njira* zanu zopezera chakudya,+ akazi 10 adzaphika mkate mu uvuni umodzi wokha, ndipo pokugawirani mkatewo, adzachita kukuyezerani+ nʼkukupatsani wochepa. Choncho mudzadya koma simudzakhuta.+
16 Kenako anandiuza kuti: “Iwe mwana wa munthu, ine ndidzachititsa kuti chakudya chisowe* mu Yerusalemu.+ Anthu azidzadya chakudya chochita kuyeza ndipo adzachidya ali ndi nkhawa yaikulu.+ Azidzamwa madzi ochita kuyeza ali ndi mantha aakulu.+
10 Iwo adzadya, koma sadzakhuta.+ Adzachita zachiwerewere, koma sadzachulukana,+Chifukwa chakuti sakumvera Yehova.