Salimo 103:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mofanana ndi mmene kotulukira dzuwa kwatalikirana ndi kolowera dzuwa,Mulungu waikanso zolakwa zathu kutali ndi ife.+ Yesaya 55:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Munthu woipa asiye njira yake+Ndipo wopweteka anzake asiye maganizo ake.Iye abwerere kwa Yehova ndipo adzamuchitira chifundo.+Abwerere kwa Mulungu wathu, chifukwa adzamukhululukira ndi mtima wonse.+ Yeremiya 31:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 “Munthu sadzaphunzitsanso mnzake kapena mʼbale wake kuti, ‘Mumʼdziwe Yehova!’+ chifukwa aliyense adzandidziwa kuyambira wamngʼono mpaka wamkulu,”+ akutero Yehova. “Ine ndidzawakhululukira zolakwa zawo ndipo machimo awo sindidzawakumbukiranso.”+
12 Mofanana ndi mmene kotulukira dzuwa kwatalikirana ndi kolowera dzuwa,Mulungu waikanso zolakwa zathu kutali ndi ife.+
7 Munthu woipa asiye njira yake+Ndipo wopweteka anzake asiye maganizo ake.Iye abwerere kwa Yehova ndipo adzamuchitira chifundo.+Abwerere kwa Mulungu wathu, chifukwa adzamukhululukira ndi mtima wonse.+
34 “Munthu sadzaphunzitsanso mnzake kapena mʼbale wake kuti, ‘Mumʼdziwe Yehova!’+ chifukwa aliyense adzandidziwa kuyambira wamngʼono mpaka wamkulu,”+ akutero Yehova. “Ine ndidzawakhululukira zolakwa zawo ndipo machimo awo sindidzawakumbukiranso.”+