-
1 Mafumu 21:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Ahabu anauza Naboti kuti: “Ndipatse munda wako wa mpesawu kuti ndizilimamo masamba, chifukwa uli pafupi ndi nyumba yanga. Mʼmalo mwa munda wakowu ndikupatsa munda wina wa mpesa, wabwino kuposa umenewu. Kapena ngati ungafune, ndiugula ndi ndalama.”
-