Yeremiya 13:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Perekani ulemerero kwa Yehova Mulungu wanuAsanabweretse mdima,Komanso mapazi anu asanapunthwe pamapiri madzulo dzuwa litalowa. Mudzayembekezera kuwala,Koma iye adzabweretsa mdima waukulu,Ndipo adzachititsa kuti mdimawo ukhale wandiweyani.+
16 Perekani ulemerero kwa Yehova Mulungu wanuAsanabweretse mdima,Komanso mapazi anu asanapunthwe pamapiri madzulo dzuwa litalowa. Mudzayembekezera kuwala,Koma iye adzabweretsa mdima waukulu,Ndipo adzachititsa kuti mdimawo ukhale wandiweyani.+