Yeremiya 26:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Mika+ wa ku Moreseti nayenso ankanenera mʼmasiku a Mfumu Hezekiya+ ya ku Yuda. Iye ankauza anthu onse a ku Yuda kuti, ‘Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti: “Ziyoni adzalimidwa ngati munda,Yerusalemu adzakhala mabwinja,+Ndipo phiri la nyumba ya Mulungu* lidzakhala ngati zitunda zamunkhalango.”’+
18 “Mika+ wa ku Moreseti nayenso ankanenera mʼmasiku a Mfumu Hezekiya+ ya ku Yuda. Iye ankauza anthu onse a ku Yuda kuti, ‘Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti: “Ziyoni adzalimidwa ngati munda,Yerusalemu adzakhala mabwinja,+Ndipo phiri la nyumba ya Mulungu* lidzakhala ngati zitunda zamunkhalango.”’+