Salimo 5:4, 5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chifukwa inu si Mulungu amene amasangalala ndi zoipa,+Palibe munthu woipa amene angakhale ndi inu.+ 5 Palibe anthu odzikuza amene angaime pamaso panu. Mumadana ndi anthu onse amene amachita zoipa.+
4 Chifukwa inu si Mulungu amene amasangalala ndi zoipa,+Palibe munthu woipa amene angakhale ndi inu.+ 5 Palibe anthu odzikuza amene angaime pamaso panu. Mumadana ndi anthu onse amene amachita zoipa.+