Salimo 137:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iwe mwana wamkazi wa Babulo,* amene watsala pangʼono kuwonongedwa,+Wosangalala adzakhala amene adzakubwezereZimene iwe watichitira.+ Yeremiya 50:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Kukumveka phokoso la anthu amene akuthawa,Amene apulumuka mʼdziko la Babulo,Kuti akanene ku Ziyoni kuti Yehova Mulungu wathu akubwezera adani ake.Akuwabwezera chifukwa cha kuwonongedwa kwa kachisi wake.+ Yeremiya 51:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndidzabwezera Babulo ndi anthu onse amene akukhala mʼdziko la KasidiChifukwa cha zoipa zonse zimene anachita ku Ziyoni inu mukuona,”+ akutero Yehova.
8 Iwe mwana wamkazi wa Babulo,* amene watsala pangʼono kuwonongedwa,+Wosangalala adzakhala amene adzakubwezereZimene iwe watichitira.+
28 Kukumveka phokoso la anthu amene akuthawa,Amene apulumuka mʼdziko la Babulo,Kuti akanene ku Ziyoni kuti Yehova Mulungu wathu akubwezera adani ake.Akuwabwezera chifukwa cha kuwonongedwa kwa kachisi wake.+
24 Ndidzabwezera Babulo ndi anthu onse amene akukhala mʼdziko la KasidiChifukwa cha zoipa zonse zimene anachita ku Ziyoni inu mukuona,”+ akutero Yehova.