Ekisodo 14:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Iye ankagulula mawilo a magaleta awo moti ankawayendetsa movutikira. Ndipo Aiguputo ankanena kuti: “Tiyeni tithawe pamaso pa Isiraeli, chifukwa Yehova akuwamenyera nkhondo yolimbana ndi Aiguputo.”+ Ekisodo 23:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Inu musanafike, ndidzawachititsa kuti azindiopa.+ Ndidzasokoneza anthu onse amene mudzakumane nawo. Ndipo ndidzachititsa kuti adani anu onse agonje nʼkuthawa.*+
25 Iye ankagulula mawilo a magaleta awo moti ankawayendetsa movutikira. Ndipo Aiguputo ankanena kuti: “Tiyeni tithawe pamaso pa Isiraeli, chifukwa Yehova akuwamenyera nkhondo yolimbana ndi Aiguputo.”+
27 Inu musanafike, ndidzawachititsa kuti azindiopa.+ Ndidzasokoneza anthu onse amene mudzakumane nawo. Ndipo ndidzachititsa kuti adani anu onse agonje nʼkuthawa.*+