Yeremiya 22:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndinalankhula nawe pamene unkaona kuti ndiwe wotetezeka. Koma iwe unanena kuti, ‘Sindimvera.’+ Wakhala ukuchita zimenezi kuyambira uli wachinyamata,Chifukwa wakhala usakumvera mawu anga.+ Yeremiya 32:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Iwo analowa mʼdzikoli nʼkulitenga kuti likhale lawo, koma sanamvere mawu anu kapena kuyenda motsatira malamulo anu. Iwo sanachite zinthu zonse zimene munawalamula kuti achite, nʼchifukwa chake munawagwetsera masoka onsewa.+
21 Ndinalankhula nawe pamene unkaona kuti ndiwe wotetezeka. Koma iwe unanena kuti, ‘Sindimvera.’+ Wakhala ukuchita zimenezi kuyambira uli wachinyamata,Chifukwa wakhala usakumvera mawu anga.+
23 Iwo analowa mʼdzikoli nʼkulitenga kuti likhale lawo, koma sanamvere mawu anu kapena kuyenda motsatira malamulo anu. Iwo sanachite zinthu zonse zimene munawalamula kuti achite, nʼchifukwa chake munawagwetsera masoka onsewa.+