Salimo 78:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Chifukwa chakuti sanakhulupirire Mulungu.+Sanakhulupirire kuti iye angathe kuwapulumutsa. Yeremiya 17:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yehova wanena kuti: “Wotembereredwa ndi munthu amene amakhulupirira munthu mnzake.+Wotembereredwa ndi munthu amene amadalira mphamvu za munthu,+Komanso amene mtima wake wapatuka kuchoka kwa Yehova.
5 Yehova wanena kuti: “Wotembereredwa ndi munthu amene amakhulupirira munthu mnzake.+Wotembereredwa ndi munthu amene amadalira mphamvu za munthu,+Komanso amene mtima wake wapatuka kuchoka kwa Yehova.