-
2 Mafumu 23:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Mfumuyo inachotsa ntchito ansembe a milungu yachilendo amene mafumu a Yuda anawaika kuti azipereka nsembe zautsi pamalo okwezeka mʼmizinda ya Yuda ndi malo ozungulira Yerusalemu. Inachotsanso ntchito ansembe opereka nsembe zautsi kwa Baala, kwa dzuwa, kwa mwezi, kwa magulu a nyenyezi ndiponso kwa gulu lonse la zinthu zakuthambo.+
-