Ekisodo 40:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Mose sanathenso kulowa mʼchihema chokumanako, chifukwa mtambo unali utaphimba chihemacho ndipo munadzaza ulemerero wa Yehova.+ 1 Mafumu 8:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chifukwa cha mtambowo, ansembewo analephera kutumikira popeza ulemerero wa Yehova unadzaza nyumba ya Yehovayo.+ Yesaya 66:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Chifukwa Yehova wanena kuti: “Ndikumupatsa mtendere ngati mtsinje+Komanso ulemerero wa mitundu ya anthu ngati mtsinje wosefukira.+ Inu mudzayamwa komanso adzakunyamulani mʼmanja,Ndipo adzakudumphitsani pamiyendo.
35 Mose sanathenso kulowa mʼchihema chokumanako, chifukwa mtambo unali utaphimba chihemacho ndipo munadzaza ulemerero wa Yehova.+
11 Chifukwa cha mtambowo, ansembewo analephera kutumikira popeza ulemerero wa Yehova unadzaza nyumba ya Yehovayo.+
12 Chifukwa Yehova wanena kuti: “Ndikumupatsa mtendere ngati mtsinje+Komanso ulemerero wa mitundu ya anthu ngati mtsinje wosefukira.+ Inu mudzayamwa komanso adzakunyamulani mʼmanja,Ndipo adzakudumphitsani pamiyendo.