Yeremiya 31:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 “Ndinkawayangʼanitsitsa kuti ndiwazule, ndiwagwetse, ndiwapasule, ndiwawononge komanso kuti ndiwasakaze.+ Mofanana ndi zimenezi, ndidzawayangʼanitsitsanso kuti ndiwamange komanso ndiwadzale,”+ akutero Yehova. Yeremiya 32:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 “Yehova wanena kuti, ‘Mofanana ndi mmene ndabweretsera anthu awa masoka aakulu onsewa, ndidzawabweretseranso zinthu zabwino zonse zimene ndikuwalonjezazi.+
28 “Ndinkawayangʼanitsitsa kuti ndiwazule, ndiwagwetse, ndiwapasule, ndiwawononge komanso kuti ndiwasakaze.+ Mofanana ndi zimenezi, ndidzawayangʼanitsitsanso kuti ndiwamange komanso ndiwadzale,”+ akutero Yehova.
42 “Yehova wanena kuti, ‘Mofanana ndi mmene ndabweretsera anthu awa masoka aakulu onsewa, ndidzawabweretseranso zinthu zabwino zonse zimene ndikuwalonjezazi.+