Deuteronomo 20:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “Mukapita kunkhondo kukamenyana ndi adani anu, nʼkuona kuti ali ndi mahatchi, magaleta ankhondo komanso asilikali ochuluka kuposa inu, musachite nawo mantha chifukwa Yehova Mulungu wanu, amene anakutulutsani mʼdziko la Iguputo ali ndi inu.+
20 “Mukapita kunkhondo kukamenyana ndi adani anu, nʼkuona kuti ali ndi mahatchi, magaleta ankhondo komanso asilikali ochuluka kuposa inu, musachite nawo mantha chifukwa Yehova Mulungu wanu, amene anakutulutsani mʼdziko la Iguputo ali ndi inu.+