-
Ezekieli 38:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Ndithu ndidzasonyeza mphamvu zanga, komanso ndidzasonyeza kuti ndine Mulungu woyera ndipo ndidzachititsa kuti anthu ambiri a mitundu ina andidziwe. Iwo adzadziwa kuti ine ndine Yehova.’”
-