10 Komabe, tsiku la Yehova+ lidzafika ngati wakuba,+ pamene kumwamba kudzachoka+ ndi mkokomo waukulu. Ndipo zinthu zimene zimapanga kumwamba ndi dziko lapansi zidzatentha kwambiri nʼkusungunuka, moti dziko lapansi ndi ntchito zake zidzaonekera poyera.+