Yesaya 42:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Taonani mtumiki wanga+ amene ndikumuthandiza, Wosankhidwa wanga+ amene amandisangalatsa,+ Ine ndaika mzimu wanga mwa iye.+Iye adzabweretsa chilungamo kwa anthu a mitundu ina.+ Yesaya 52:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Taona! Mtumiki wanga+ azidzachita zinthu mwanzeru. Adzapatsidwa udindo wapamwambaAdzakwezedwa ndipo adzalemekezedwa kwambiri.+
42 Taonani mtumiki wanga+ amene ndikumuthandiza, Wosankhidwa wanga+ amene amandisangalatsa,+ Ine ndaika mzimu wanga mwa iye.+Iye adzabweretsa chilungamo kwa anthu a mitundu ina.+
13 Taona! Mtumiki wanga+ azidzachita zinthu mwanzeru. Adzapatsidwa udindo wapamwambaAdzakwezedwa ndipo adzalemekezedwa kwambiri.+