Levitiko 22:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Musamapereke nsembe nyama iliyonse yachilema,+ chifukwa Mulungu sangasangalale nanu. Levitiko 22:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Isakhale yakhungu, yothyoka fupa, yotemeka, yokhala ndi njerewere, nkhanambo* kapena zipere. Musamapereke kwa Yehova nyama zoterezi kapena kuwotcha nyama zoterezi paguwa lansembe la Yehova. Deuteronomo 15:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Koma ngati nyamayo ili ndi vuto, monga kulumala kapena khungu, kapena chilema chilichonse chachikulu, musamaipereke nsembe kwa Yehova Mulungu wanu.+
22 Isakhale yakhungu, yothyoka fupa, yotemeka, yokhala ndi njerewere, nkhanambo* kapena zipere. Musamapereke kwa Yehova nyama zoterezi kapena kuwotcha nyama zoterezi paguwa lansembe la Yehova.
21 Koma ngati nyamayo ili ndi vuto, monga kulumala kapena khungu, kapena chilema chilichonse chachikulu, musamaipereke nsembe kwa Yehova Mulungu wanu.+