Deuteronomo 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Taonani, ndakuuzani malangizo ndi zigamulo,+ mogwirizana ndi zimene Yehova Mulungu wanga wandilamula, kuti muzikatsatira zimenezo mʼdziko limene mukupita kukalitenga kuti likhale lanu.
5 Taonani, ndakuuzani malangizo ndi zigamulo,+ mogwirizana ndi zimene Yehova Mulungu wanga wandilamula, kuti muzikatsatira zimenezo mʼdziko limene mukupita kukalitenga kuti likhale lanu.