Mateyu 13:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 ndipo mdani amene anafesa namsongole ndi Mdyerekezi. Nthawi yokolola ikuimira mapeto a nthawi* ino ndipo okololawo ndi angelo. Mateyu 13:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Ndi mmenenso zidzakhalire pamapeto a nthawi* ino. Angelo adzapita nʼkukachotsa oipa pakati pa olungama Mateyu 24:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Atakhala pansi mʼphiri la Maolivi, ophunzira anabwera kwa iye ali payekha nʼkumufunsa kuti: “Tiuzeni, kodi zinthu zimenezi zidzachitika liti, ndipo chizindikiro cha kukhalapo* kwanu+ ndi cha mapeto a nthawi* ino+ chidzakhala chiyani?”
39 ndipo mdani amene anafesa namsongole ndi Mdyerekezi. Nthawi yokolola ikuimira mapeto a nthawi* ino ndipo okololawo ndi angelo.
49 Ndi mmenenso zidzakhalire pamapeto a nthawi* ino. Angelo adzapita nʼkukachotsa oipa pakati pa olungama
3 Atakhala pansi mʼphiri la Maolivi, ophunzira anabwera kwa iye ali payekha nʼkumufunsa kuti: “Tiuzeni, kodi zinthu zimenezi zidzachitika liti, ndipo chizindikiro cha kukhalapo* kwanu+ ndi cha mapeto a nthawi* ino+ chidzakhala chiyani?”