Mateyu 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mukamakhululukira anthu machimo awo, inunso Atate wanu wakumwamba adzakukhululukirani.+ Mateyu 18:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Kodi sukanamuchitira chifundo kapolo mnzako, ngati mmene ine ndachitira kwa iwe?’+ Yakobo 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chifukwa munthu amene sasonyeza chifundo adzaweruzidwa mopanda chifundo.+ Chifundo nʼchachikulu kuposa chiweruzo.
13 Chifukwa munthu amene sasonyeza chifundo adzaweruzidwa mopanda chifundo.+ Chifundo nʼchachikulu kuposa chiweruzo.