1 Mafumu 15:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kenako Asa, mofanana ndi makolo ake, anamwalira ndipo anaikidwa mʼmanda a makolo ake mu Mzinda wa Davide kholo lake. Ndiyeno mwana wake Yehosafati+ anakhala mfumu mʼmalo mwake.
24 Kenako Asa, mofanana ndi makolo ake, anamwalira ndipo anaikidwa mʼmanda a makolo ake mu Mzinda wa Davide kholo lake. Ndiyeno mwana wake Yehosafati+ anakhala mfumu mʼmalo mwake.