Levitiko 19:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Usabwezere choipa+ kapena kusungira chakukhosi anthu a mtundu wako. Uzikonda mnzako mmene umadzikondera wekha.+ Ine ndine Yehova. Maliko 12:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Lachiwiri ndi ili, ‘Uzikonda mnzako mmene umadzikondera wekha.’+ Palibe lamulo lina lalikulu kuposa amenewa.”
18 Usabwezere choipa+ kapena kusungira chakukhosi anthu a mtundu wako. Uzikonda mnzako mmene umadzikondera wekha.+ Ine ndine Yehova.
31 Lachiwiri ndi ili, ‘Uzikonda mnzako mmene umadzikondera wekha.’+ Palibe lamulo lina lalikulu kuposa amenewa.”