Yohane 14:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Komanso chilichonse chimene mudzapemphe mʼdzina langa, ine ndidzachichita, kuti Atate alemekezedwe kudzera mwa Mwana wake.+ 1 Yohane 3:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndipo chilichonse chimene tingamupemphe adzatipatsa,+ chifukwa timamvera malamulo ake komanso tikuchita zinthu zomusangalatsa.
13 Komanso chilichonse chimene mudzapemphe mʼdzina langa, ine ndidzachichita, kuti Atate alemekezedwe kudzera mwa Mwana wake.+
22 Ndipo chilichonse chimene tingamupemphe adzatipatsa,+ chifukwa timamvera malamulo ake komanso tikuchita zinthu zomusangalatsa.