Yakobo 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mphatso iliyonse yabwino ndi yangwiro imachokera kumwamba.+ Imatsika kuchokera kwa Atate wa zounikira zakuthambo,+ amene sasintha ngati mthunzi umene umasunthasuntha.+
17 Mphatso iliyonse yabwino ndi yangwiro imachokera kumwamba.+ Imatsika kuchokera kwa Atate wa zounikira zakuthambo,+ amene sasintha ngati mthunzi umene umasunthasuntha.+