Aroma 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Paja anthu ongomva Chilamulo, Mulungu samawaona kuti ndi olungama koma amene amatsatira Chilamulo ndi amene adzaonedwe kuti ndi olungama.+ Yakobo 1:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Komabe muzichita zimene mawu amanena,+ osati kungomva chabe, nʼkumadzipusitsa ndi maganizo abodza. 1 Yohane 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kuwonjezera pamenepa, dzikoli likupita ndiponso chilichonse cha mʼdzikoli chimene anthu amalakalaka chikupita.+ Koma wochita zimene Mulungu amafuna adzakhala mpaka kalekale.+ 1 Yohane 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kukonda Mulungu kumatanthauza kutsatira malamulo ake,+ ndipo malamulo akewo si ovuta kuwatsatira.+
13 Paja anthu ongomva Chilamulo, Mulungu samawaona kuti ndi olungama koma amene amatsatira Chilamulo ndi amene adzaonedwe kuti ndi olungama.+
22 Komabe muzichita zimene mawu amanena,+ osati kungomva chabe, nʼkumadzipusitsa ndi maganizo abodza.
17 Kuwonjezera pamenepa, dzikoli likupita ndiponso chilichonse cha mʼdzikoli chimene anthu amalakalaka chikupita.+ Koma wochita zimene Mulungu amafuna adzakhala mpaka kalekale.+