Luka 9:59 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 59 Kenako anauza munthu wina kuti: “Ukhale wotsatira wanga.” Koma munthuyo anati: “Ambuye, ndiloleni ndiyambe ndapita kukaika maliro a bambo anga.”+
59 Kenako anauza munthu wina kuti: “Ukhale wotsatira wanga.” Koma munthuyo anati: “Ambuye, ndiloleni ndiyambe ndapita kukaika maliro a bambo anga.”+