Luka 1:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Poyankha mngeloyo anauza Mariya kuti: “Mzimu woyera udzafika pa iwe+ ndipo mphamvu ya Wamʼmwambamwamba idzakuphimba. Pa chifukwa chimenechi amene adzabadweyo adzatchedwa woyera,+ Mwana wa Mulungu.+
35 Poyankha mngeloyo anauza Mariya kuti: “Mzimu woyera udzafika pa iwe+ ndipo mphamvu ya Wamʼmwambamwamba idzakuphimba. Pa chifukwa chimenechi amene adzabadweyo adzatchedwa woyera,+ Mwana wa Mulungu.+