-
Mateyu 12:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Kenako anamubweretsera munthu wogwidwa ndi chiwanda, amenenso anali ndi vuto losaona komanso sankalankhula ndipo iye anamuchiritsa, moti munthu wosalankhulayo anayamba kulankhula ndiponso kuona.
-